PULUMUTSANI MOYO
*PULUMUTSANI MOYO*
😴Panopa Kukuzidzira Kwambiri pa chifukwa cha ichi, thupi limapanga manyazi kuitanitsa madzi akumwa koma ife tisalimvere maganidzo akewo, ngati tingamvere tikumana ndi mavuto awa:😴
1) Kumva kuwawa pokodza.
2) Ma kidney athu amasunga miyala nkati mwake.
3) M'thupi muzakhala mafuta ochuluka kwambili koma ali Owundanda.
4) Kupuma kumakhala kovutirapo.
5) Magazi sapangika mokwanira.
😴Ndiyeno tisadikire kuti tidwale kaye, imwani madzi okwanira bolako 2ltrs or 3ltrs per day.
Zindikirani kuti madzi ndi moyo. Tikamayankhula muja timakhala tikutaya madzi, pumirani pa galasi mupedza galasi la nyowa anyowetsa aja ndi madzi, tiyeni tipewe mavuto odza kamba kakuzidzira.
👉Tisafunde mutu chifukwa cha kuzidzira ayi ubongo umafuna oxygen wochuluka pamene tikugona.
👉Tiyeni tidzidya zakudya zotentha nthawi zonse panyengoi Kuti tikapewe kuwundana kwa mafuta m'thupi.
*😴Chifukwa cha kuzidziraku ambili azikumana ndi vuto la Kkuwawa kwa mutu komanso Flue Chimfine😴* Tiyeni timwe juice wa mandimu,ginger, bluegum, kufikira titadutsa nyengo imeneyi.😴
Zikomo kwambiri aliyense payekha payekha Mulungu amukute pa nthawi yomwe tonse Tili pano pa dziko lapansi.😴
*Tsiku labwino🙏🙏*
Ndine Victor Kaludzu
Comments
Post a Comment