Kodi mukanavutikabe ndikuzima zima kwamagetsi ai ndithu azanutu imeneija ndimbiri yakale ndipo akusimba zina pano ndi SOLARWORKS kudana ndi M'dima Pezani anu magetsi a menewa kwaife pangongole kapena kugula cash kutengera ndi nthumba mwanu. Pezani set ya Solar Yongounikira ndiku charge ma phone Set yama Bulb 4, Radio and Touch Pangongole Deposit 18,000 pamwezi 13,000 kwamiyezi 30 kapena 16,000 pamwezi kwamiyezi 18 Cash ndi 195,000 Set ya SOLAR and PLASMA 24 inch Deposit 60,000 pamwezi 32,000 kwamiyezi 30 kuunikira , kuonelera ndiku charge ma phone Kapena 42,000 pamwezi kwamiyezi 18 Cash 530,000 Set ya SOLAR and PLASMA 32 inch Deposit 70,000 pamwezi 42,000 kwamiyezi 30 Kuunikira, kuonelera ndiku charge ma phone Kapena 51,000 pamwezi kwamiyezi 18 Cash ndi 780,000 Guarantee 2 years Kupanga installation ndi ulele Pezani yanu set imeneyi kapena apezeleni Makolo kumudzi Musachedwe kunoku Lilongwe taimba pa 0991524049 Mudzathandizika mosavuta.