SOLAR WORKS
Kodi mukanavutikabe ndikuzima zima kwamagetsi ai ndithu azanutu imeneija ndimbiri yakale ndipo akusimba zina pano ndi SOLARWORKS kudana ndi M'dima
Pezani anu magetsi a menewa kwaife pangongole kapena kugula cash kutengera ndi nthumba mwanu.
Pezani set ya Solar Yongounikira ndiku charge ma phone
Set yama Bulb 4, Radio and Touch
Pangongole Deposit 18,000 pamwezi 13,000 kwamiyezi 30 kapena 16,000 pamwezi kwamiyezi 18
Cash ndi 195,000
Set ya SOLAR and PLASMA 24 inch Deposit 60,000 pamwezi 32,000 kwamiyezi 30 kuunikira , kuonelera ndiku charge ma phone
Kapena 42,000 pamwezi kwamiyezi 18
Cash 530,000
Set ya SOLAR and PLASMA 32 inch Deposit 70,000 pamwezi 42,000 kwamiyezi 30
Kuunikira, kuonelera ndiku charge ma phone
Kapena 51,000 pamwezi kwamiyezi 18
Cash ndi 780,000
Guarantee 2 years
Kupanga installation ndi ulele
Pezani yanu set imeneyi kapena apezeleni Makolo kumudzi
Musachedwe kunoku Lilongwe taimba pa 0991524049
Mudzathandizika mosavuta.
Comments
Post a Comment